Maliko 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma popeza kuti sanathe kum’fikitsa kwa Yesu chifukwa cha kuchuluka kwa anthu, anasasula denga* pamene iye anali, ndipo ataboola padengapo, anatsitsirapo machira a munthu wakufa ziwalo uja.+
4 Koma popeza kuti sanathe kum’fikitsa kwa Yesu chifukwa cha kuchuluka kwa anthu, anasasula denga* pamene iye anali, ndipo ataboola padengapo, anatsitsirapo machira a munthu wakufa ziwalo uja.+