Mateyu 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma akakuperekani kumeneko, musade nkhawa za mmene mukalankhulire kapena zimene mukanene. Mudzapatsidwa nthawi yomweyo zoti mulankhule,+ Luka 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akapita nanu kumabwalo amilandu, ndi kwa akuluakulu aboma, komanso kwa olamulira, musade nkhawa kuti mukadziteteza bwanji kapena mukanena chiyani.+ Luka 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero tsimikizirani m’mitima yanu kuti musachite kukonzekera zoti mukayankhe podziteteza,+
19 Koma akakuperekani kumeneko, musade nkhawa za mmene mukalankhulire kapena zimene mukanene. Mudzapatsidwa nthawi yomweyo zoti mulankhule,+
11 Akapita nanu kumabwalo amilandu, ndi kwa akuluakulu aboma, komanso kwa olamulira, musade nkhawa kuti mukadziteteza bwanji kapena mukanena chiyani.+