Mateyu 24:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Tsopano phunzirani mfundo imeneyi pa fanizo ili la mkuyu: Nthambi yake yanthete ikaphuka ndi kuchita masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi.+ Luka 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Atanena izi, anawauza fanizo kuti: “Onetsetsani mtengo wa mkuyu ndi mitengo ina yonse:+
32 “Tsopano phunzirani mfundo imeneyi pa fanizo ili la mkuyu: Nthambi yake yanthete ikaphuka ndi kuchita masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi.+