Deuteronomo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+ Yohane 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti osaukawo+ muli nawo nthawi zonse, koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.”
11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+