Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 9:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Atatulutsa chiwandacho, munthu wosalankhulayo analankhula,+ moti khamu la anthulo linadabwa+ ndipo linanena kuti: “Zinthu zoterezi sizinaonekepo n’kale lonse mu Isiraeli.”

  • Yohane 7:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Komabe ochuluka m’khamu la anthulo anakhulupirira mwa iye+ ndipo anayamba kunena kuti: “Akadzafika Khristu, kodi adzachita zizindikiro zochuluka+ kuposa zimene munthu uyu wachita?”

  • Yohane 9:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Sizinamveke n’kale lonse kuti wina watsegula maso a munthu amene anabadwa wakhungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena