Yohane 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 koma kuti dziko lidziwe kuti ndimakonda Atate, ndikuchita izi kutsatira lamulo+ limene Atatewo anandipatsa. Nyamukani, tiyeni tichokeko kuno.
31 koma kuti dziko lidziwe kuti ndimakonda Atate, ndikuchita izi kutsatira lamulo+ limene Atatewo anandipatsa. Nyamukani, tiyeni tichokeko kuno.