Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Palibe munthu amene akuuchotsa kwa ine, koma ndikuupereka mwa kufuna kwanga. Ndili ndi mphamvu zoupereka, ndiponso ndili ndi mphamvu zoulandiranso.+ Atate wanga ndi amene anandilamula+ kuchita zimenezi.”

  • Yohane 12:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Chifukwa sindinalankhulepo zongoganiza pandekha, koma Atate amene ananditumawo anandipatsa lamulo pa zimene ndiyenera kunena ndi zimene ndiyenera kulankhula.+

  • Yohane 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mukasunga malamulo anga,+ mudzakhalabe m’chikondi changa, monga mmene ine ndasungira malamulo a Atate+ ndi kukhalabe m’chikondi chake.

  • Afilipi 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kuposanso pamenepo, atakhala munthu,+ anadzichepetsa ndi kukhala womvera mpaka imfa.+ Anakhala womvera mpaka imfa ya pamtengo wozunzikirapo.*+

  • 1 Yohane 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena