Mateyu 26:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Apa n’kuti womupereka ameneyu atawapatsa chizindikiro chakuti: “Amene ndim’psompsone ndi ameneyo, mum’gwire.”+
48 Apa n’kuti womupereka ameneyu atawapatsa chizindikiro chakuti: “Amene ndim’psompsone ndi ameneyo, mum’gwire.”+