Maliko 14:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Apa n’kuti womupereka ameneyu atawapatsa chizindikiro chimene anagwirizana nawo, chakuti: “Amene ndim’psompsone ndi ameneyo. Mum’gwire ndi kupita naye osam’taya.”+
44 Apa n’kuti womupereka ameneyu atawapatsa chizindikiro chimene anagwirizana nawo, chakuti: “Amene ndim’psompsone ndi ameneyo. Mum’gwire ndi kupita naye osam’taya.”+