Luka 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano okhometsa msonkho+ komanso anthu ochimwa,+ onse anali kubwera kwa iye kudzamumvetsera.