Mateyu 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye sali pano chifukwa wauka kwa akufa+ monga ananenera. Bwerani muone pamene anagona.