Luka 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno ali m’nyumbayo n’kuyankha kuti, ‘Usandivutitse ine.+ Takhoma kale chitseko, ndipo ine ndi ana anga tagona kale. Sindingadzukenso kuti ndikupatse kanthu.’
7 Ndiyeno ali m’nyumbayo n’kuyankha kuti, ‘Usandivutitse ine.+ Takhoma kale chitseko, ndipo ine ndi ana anga tagona kale. Sindingadzukenso kuti ndikupatse kanthu.’