Mateyu 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Woyamba anam’patsa ndalama zokwana matalente asanu, wachiwiri anam’patsa matalente awiri, ndipo wachitatu anam’patsa talente imodzi. Aliyense anam’patsa malinga ndi luso lake,+ ndipo iye anapita kudziko lina.
15 Woyamba anam’patsa ndalama zokwana matalente asanu, wachiwiri anam’patsa matalente awiri, ndipo wachitatu anam’patsa talente imodzi. Aliyense anam’patsa malinga ndi luso lake,+ ndipo iye anapita kudziko lina.