Mateyu 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Woyamba anamupatsa ndalama zokwana matalente* 5, wachiwiri anamupatsa matalente awiri ndipo wachitatu anamupatsa talente imodzi. Aliyense anamupatsa mogwirizana ndi luso lake ndipo iye anapita kudziko lina. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:15 Nsanja ya Olonda,3/15/2015, ptsa. 20-213/1/2004, ptsa. 15-166/15/1995, ptsa. 17-18 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 57, 58-60, 64
15 Woyamba anamupatsa ndalama zokwana matalente* 5, wachiwiri anamupatsa matalente awiri ndipo wachitatu anamupatsa talente imodzi. Aliyense anamupatsa mogwirizana ndi luso lake ndipo iye anapita kudziko lina.
25:15 Nsanja ya Olonda,3/15/2015, ptsa. 20-213/1/2004, ptsa. 15-166/15/1995, ptsa. 17-18 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 57, 58-60, 64