Mateyu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ansembe aakulu ndi alembi ataona zodabwitsa zimene anachitazo+ komanso anyamata amene anali kufuula m’kachisimo kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!”+ anakwiya kwambiri Yohane 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Afarisi+ anayamba kuuzana kuti: “Apa ndiye mukudzionera nokha kuti palibiretu chimene tikuphulapo. Onani! Dziko lonse lakhamukira kwa iye.”+
15 Ansembe aakulu ndi alembi ataona zodabwitsa zimene anachitazo+ komanso anyamata amene anali kufuula m’kachisimo kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!”+ anakwiya kwambiri
19 Pamenepo Afarisi+ anayamba kuuzana kuti: “Apa ndiye mukudzionera nokha kuti palibiretu chimene tikuphulapo. Onani! Dziko lonse lakhamukira kwa iye.”+