Habakuku 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwala wa pakhoma* udzalira mwachisoni ndipo kuchokera padenga* mtanda wa denga udzayankha.+ Mateyu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamadzinyenge kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu angathe kuutsira Abulahamu+ ana kuchokera kumiyala iyi.
9 Musamadzinyenge kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu angathe kuutsira Abulahamu+ ana kuchokera kumiyala iyi.