Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Machitidwe 13:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pamene anthu a mitundu inawo anamva zimenezi, anakondwera ndi kutamanda mawu a Yehova.+ Ndipo onse amene anali ndi maganizo abwino amene akanawathandiza kukapeza moyo wosatha anakhala okhulupirira.+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
48 Pamene anthu a mitundu inawo anamva zimenezi, anakondwera ndi kutamanda mawu a Yehova.+ Ndipo onse amene anali ndi maganizo abwino amene akanawathandiza kukapeza moyo wosatha anakhala okhulupirira.+