Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 39:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano Yesaya anauza Hezekiya kuti:+ “Imvani mawu a Yehova wa makamu.

  • Yesaya 66:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Inu amene mukunjenjemera ndi mawu ake, imvani mawu a Yehova:+ “Abale anu amene akudana nanu,+ amene akukusalani chifukwa cha dzina langa,+ anati, ‘Alemekezeke Yehova!’+ Mulungu adzaonekera ndipo inu mudzasangalala,+ koma iwowo ndi amene adzachite manyazi.”+

  • Machitidwe 11:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tsopano pamene iwo anamva zimenezi, anangovomereza,+ ndipo anatamanda Mulungu+ kuti: “Chabwino, pamenepa ndiye kuti Mulungu wapereka mwayi kwa anthu a mitundu ina kuti iwonso alape ndi kudzapeza moyo.”+

  • 2 Atesalonika 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 kuti dzina la Ambuye wathu Yesu lilemekezeke mwa inu,+ ndi inu mwa iye,+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu wathu, ndi kwa Ambuye Yesu Khristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena