Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano tiyeni tichite pangano+ ndi Mulungu wathu, lakuti tisiya+ akazi onse amenewa ndi ana awo mogwirizana ndi lamulo la Yehova ndi la anthu amene akunjenjemera+ chifukwa cha lamulo+ la Mulungu wathu, kuti zinthu zichitike mogwirizana ndi lamulo.+

  • Yesaya 66:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+

  • Yeremiya 36:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano atamva mawu onsewa anayang’anana mwamantha, ndipo anauza Baruki kuti: “Ndithu, tikauza mfumu mawu onsewa.”+

  • Habakuku 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nditamva mawu ake, m’mimba mwanga munayamba kubwadamuka ndipo milomo yanga inanjenjemera. Mafupa anga anayamba kuwola+ ndipo ndinanthunthumira chifukwa cha mmene zinthu zinalili. Choncho ndidzayembekezera mofatsa tsiku la nsautso.+ Tsiku limeneli lidzabwera kwa anthu+ ngati mmene munthu amabwerera kwa adani ake kuti awaukire.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena