Salimo 119:120 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+ Yeremiya 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mtima wanga wasweka mkati mwanga chifukwa cha aneneri. Mafupa anga onse ayamba kunjenjemera. Ndakhala ngati munthu woledzera,+ komanso mwamuna wamphamvu amene wagonjetsedwa ndi vinyo, chifukwa cha Yehova komanso chifukwa cha mawu ake oyera. Danieli 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno ineyo Danieli ndinatopa kwambiri ndipo ndinadwala kwa masiku angapo.+ Kenako ndinadzuka ndi kugwira ntchito yotumikira mfumu.+ Koma ndinali wodabwa kwambiri ndi zimene ndinaona, ndipo palibe amene anazimvetsa.+
120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+
9 Mtima wanga wasweka mkati mwanga chifukwa cha aneneri. Mafupa anga onse ayamba kunjenjemera. Ndakhala ngati munthu woledzera,+ komanso mwamuna wamphamvu amene wagonjetsedwa ndi vinyo, chifukwa cha Yehova komanso chifukwa cha mawu ake oyera.
27 Ndiyeno ineyo Danieli ndinatopa kwambiri ndipo ndinadwala kwa masiku angapo.+ Kenako ndinadzuka ndi kugwira ntchito yotumikira mfumu.+ Koma ndinali wodabwa kwambiri ndi zimene ndinaona, ndipo palibe amene anazimvetsa.+