Machitidwe 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho nyumba yonse ya Isiraeli idziwe ndithu, kuti Yesu ameneyu, amene inu munam’pachika,+ Mulungu anamuika kukhala Ambuye+ ndi Khristu.” Afilipi 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kutinso aliyense avomereze poyera ndi lilime lake+ kuti Yesu Khristu ndiye Ambuye,+ polemekeza Mulungu Atate.+
36 Choncho nyumba yonse ya Isiraeli idziwe ndithu, kuti Yesu ameneyu, amene inu munam’pachika,+ Mulungu anamuika kukhala Ambuye+ ndi Khristu.”
11 Kutinso aliyense avomereze poyera ndi lilime lake+ kuti Yesu Khristu ndiye Ambuye,+ polemekeza Mulungu Atate.+