Mateyu 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa chomva chisoni kwambiri ndi zimenezi, aliyense anayamba kumufunsa kuti: “Ambuye, kodi ndine kapena?”+ Maliko 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo chisoni chinawagwira ndipo anayamba kumufunsa mmodzimmodzi kuti: “Kodi ndine kapena?”+ Yohane 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ophunzirawo anayamba kuyang’anizana posadziwa kuti anali kunena ndani.+
22 Chifukwa chomva chisoni kwambiri ndi zimenezi, aliyense anayamba kumufunsa kuti: “Ambuye, kodi ndine kapena?”+