Yohane 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ophunzirawo anayamba kuyangʼanizana chifukwa sankadziwa kuti akunena ndani.+