Yohane 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ophunzirawo anayamba kuyang’anizana posadziwa kuti anali kunena ndani.+