Luka 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Tamverani! Tsopano tikupita ku Yerusalemu, ndipo zonse zimene zinalembedwa ndi aneneri,+ zokhudza Mwana wa munthu zikakwaniritsidwa.+
31 Kenako anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Tamverani! Tsopano tikupita ku Yerusalemu, ndipo zonse zimene zinalembedwa ndi aneneri,+ zokhudza Mwana wa munthu zikakwaniritsidwa.+