Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+ Maliko 14:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atatero anachokanso kupita kukapemphera, motchula mawu omwe aja.+
39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+