Mateyu 26:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Apa n’kuti womupereka ameneyu atawapatsa chizindikiro chakuti: “Amene ndim’psompsone ndi ameneyo, mum’gwire.”+ Maliko 14:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pamenepo Yudasi anayenda molunjika ndi kufika kwa iye. Kenako anati: “Rabi!” Ndipo anam’psompsona.+
48 Apa n’kuti womupereka ameneyu atawapatsa chizindikiro chakuti: “Amene ndim’psompsone ndi ameneyo, mum’gwire.”+
45 Pamenepo Yudasi anayenda molunjika ndi kufika kwa iye. Kenako anati: “Rabi!” Ndipo anam’psompsona.+