Yesaya 53:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+ Machitidwe 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndime ya m’Malemba imene anali kuwerenga mokwezayo, mawu ake ndi awa: “Iye anamutengera kokamupha ngati nkhosa. Ngati mwana wa nkhosa wongokhala chete pamene akumumeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
32 Ndime ya m’Malemba imene anali kuwerenga mokwezayo, mawu ake ndi awa: “Iye anamutengera kokamupha ngati nkhosa. Ngati mwana wa nkhosa wongokhala chete pamene akumumeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+