Mateyu 26:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Tsopano Petulo anakhala pansi m’bwalo lamkati, ndipo mtsikana wantchito anabwera kwa iye n’kunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu wa ku Galileyayu!”+ Maliko 14:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ataona Petulo akuwotha moto, anamuyang’anitsitsa ndi kunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu, Mnazareti uja.”+
69 Tsopano Petulo anakhala pansi m’bwalo lamkati, ndipo mtsikana wantchito anabwera kwa iye n’kunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu wa ku Galileyayu!”+
67 Ataona Petulo akuwotha moto, anamuyang’anitsitsa ndi kunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu, Mnazareti uja.”+