Luka 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Herode anati: “Yohane ndinamudula mutu.+ Nanga uyu ndaninso amene akuchita zomwe ndikumvazi?” Choncho anali kufunitsitsa kumuona.+
9 Ndiyeno Herode anati: “Yohane ndinamudula mutu.+ Nanga uyu ndaninso amene akuchita zomwe ndikumvazi?” Choncho anali kufunitsitsa kumuona.+