Yohane 18:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pilato anafunsa kuti: “Choonadi n’chiyani?” Atangofunsa funso limeneli, anatuluka ndi kupitanso kumene kunali Ayuda kuja, ndi kuwauza kuti: “Ineyo sindikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+
38 Pilato anafunsa kuti: “Choonadi n’chiyani?” Atangofunsa funso limeneli, anatuluka ndi kupitanso kumene kunali Ayuda kuja, ndi kuwauza kuti: “Ineyo sindikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+