Mateyu 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poona kuti sizikuthandiza, komanso pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi+ ndi kusamba m’manja pamaso pa khamu la anthulo, n’kunena kuti: “Inetu ndasamba m’manja, ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.” Luka 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Pilato anauza ansembe aakulu ndi khamu la anthulo kuti: “Sindikupeza mlandu uliwonse mwa munthu uyu.”+ Yohane 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zili choncho kuti mawu olembedwa m’Chilamulo akwaniritsidwe. Mawu ake ndi akuti, ‘Anadana nane popanda chifukwa.’+
24 Poona kuti sizikuthandiza, komanso pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi+ ndi kusamba m’manja pamaso pa khamu la anthulo, n’kunena kuti: “Inetu ndasamba m’manja, ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.”
4 Pamenepo Pilato anauza ansembe aakulu ndi khamu la anthulo kuti: “Sindikupeza mlandu uliwonse mwa munthu uyu.”+
25 Zili choncho kuti mawu olembedwa m’Chilamulo akwaniritsidwe. Mawu ake ndi akuti, ‘Anadana nane popanda chifukwa.’+