Machitidwe 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno mzimu unauza+ Filipo kuti: “Yandikira galeta lakelo uyende naye limodzi.”