Yohane 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atanena zimenezi, anatembenuka ndi kuona Yesu ali chilili, koma sanam’zindikire kuti ndi Yesu.+ Yohane 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene kunali kucha, Yesu anaimirira m’mbali mwa nyanja, koma ophunzirawo sanazindikire kuti anali Yesu.+
4 Pamene kunali kucha, Yesu anaimirira m’mbali mwa nyanja, koma ophunzirawo sanazindikire kuti anali Yesu.+