Luka 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma m’maso mwawo sanathe kumuzindikira.+ Yohane 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atanena zimenezi, anatembenuka ndi kuona Yesu ali chilili, koma sanam’zindikire kuti ndi Yesu.+