Mateyu 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, iwo anachoka mwamsanga pamanda achikumbutsowo, ali ndi mantha ndiponso chimwemwe chochuluka, ndipo anathamanga kukauza ophunzira ake.+ Luka 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amayiwa anali Mariya Mmagadala, Jowana+ ndi Mariya mayi wa Yakobo. Komanso amayi+ ena onse amene anali nawo pamodzi anali kuuza atumwi zinthu zimenezi.
8 Choncho, iwo anachoka mwamsanga pamanda achikumbutsowo, ali ndi mantha ndiponso chimwemwe chochuluka, ndipo anathamanga kukauza ophunzira ake.+
10 Amayiwa anali Mariya Mmagadala, Jowana+ ndi Mariya mayi wa Yakobo. Komanso amayi+ ena onse amene anali nawo pamodzi anali kuuza atumwi zinthu zimenezi.