-
Luka 24:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 [[Koma Petulo ananyamuka ndi kuthamangira kumanda achikumbutsoko, ndipo atasuzumira mkati, anangoona nsalu zokulungira mtembo zokha. Choncho anachoka ali wodabwa kwambiri ndi zimene zinachitikazo.]]
-