Machitidwe 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anali kufotokoza ndi kusonyeza umboni wolembedwa powatsimikizira kuti kunali koyenera kuti Khristu avutike+ ndi kuuka kwa akufa.+ Anali kunena kuti: “Yesu amene ndikumulalikira kwa inu, ndiye Khristu.”+ 1 Akorinto 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwa zinthu zofunika kwambiri zimene ndinakupatsirani zija, zimenenso ineyo ndinalandira,+ panali zonena kuti, Khristu anafera machimo athu, malinga ndi Malemba.+
3 Iye anali kufotokoza ndi kusonyeza umboni wolembedwa powatsimikizira kuti kunali koyenera kuti Khristu avutike+ ndi kuuka kwa akufa.+ Anali kunena kuti: “Yesu amene ndikumulalikira kwa inu, ndiye Khristu.”+
3 Mwa zinthu zofunika kwambiri zimene ndinakupatsirani zija, zimenenso ineyo ndinalandira,+ panali zonena kuti, Khristu anafera machimo athu, malinga ndi Malemba.+