Mateyu 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamene ophunzirawo anamuona akuyenda panyanjapo, anavutika mumtima, n’kumanena kuti: “Amenewa ndi masomphenya ndithu!”+ Ndipo anafuula mwamantha.
26 Pamene ophunzirawo anamuona akuyenda panyanjapo, anavutika mumtima, n’kumanena kuti: “Amenewa ndi masomphenya ndithu!”+ Ndipo anafuula mwamantha.