Yohane 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chapafupi ndi mtengo wozunzikirapo wa Yesu, panaimirira mayi ake+ ndi m’bale wa mayi akewo, Mariya+ mkazi wa Kulopa, ndi Mariya Mmagadala.+
25 Koma chapafupi ndi mtengo wozunzikirapo wa Yesu, panaimirira mayi ake+ ndi m’bale wa mayi akewo, Mariya+ mkazi wa Kulopa, ndi Mariya Mmagadala.+