Mateyu 27:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Pakati pawo panali Mariya Mmagadala, Mariya mayi a Yakobo ndi Yose, ndiponso panali mayi a Yakobo ndi Yohane.*+ Maliko 15:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Panali amayi amene anali kuonerera chapatali ndithu,+ ena mwa iwo anali Mariya Mmagadala, Mariya mayi wa Yakobo Wamng’ono ndi Yose, komanso Salome,+ Luka 23:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Komanso onse amene anali kumudziwa anaimirira chapatali ndithu.+ Ndipo amayi amene anamutsatira kuchokera ku Galileya, anaimiriranso chapomwepo n’kumaonerera zinthu zimenezi.+
56 Pakati pawo panali Mariya Mmagadala, Mariya mayi a Yakobo ndi Yose, ndiponso panali mayi a Yakobo ndi Yohane.*+
40 Panali amayi amene anali kuonerera chapatali ndithu,+ ena mwa iwo anali Mariya Mmagadala, Mariya mayi wa Yakobo Wamng’ono ndi Yose, komanso Salome,+
49 Komanso onse amene anali kumudziwa anaimirira chapatali ndithu.+ Ndipo amayi amene anamutsatira kuchokera ku Galileya, anaimiriranso chapomwepo n’kumaonerera zinthu zimenezi.+