Mateyu 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nkhwangwa+ yaikidwa kale pamizu yamitengo. Chotero mtengo uliwonse wosabala zipatso zabwino udulidwa+ ndi kuponyedwa pamoto.+ Mateyu 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mtengo uliwonse wosabala zipatso zabwino amaudula ndi kuuponya pamoto.+ Yohane 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+
10 Nkhwangwa+ yaikidwa kale pamizu yamitengo. Chotero mtengo uliwonse wosabala zipatso zabwino udulidwa+ ndi kuponyedwa pamoto.+
6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+