Mateyu 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Herode anagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+
3 Pakuti Herode anagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+