Mateyu 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Yesu atamva kuti Yohane amugwira,+ anachoka kumeneko ndipo anapita ku Galileya.+ Maliko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Herodeyo anatumiza anthu kukagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende, chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+ Luka 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno popeza kuti Yohane anadzudzula Herode wolamulira chigawo, pa nkhani yokhudza Herodiya, mkazi wa m’bale wake, komanso chifukwa cha zoipa zonse zimene Herode anachita,+
17 Pakuti Herodeyo anatumiza anthu kukagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende, chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+
19 Ndiyeno popeza kuti Yohane anadzudzula Herode wolamulira chigawo, pa nkhani yokhudza Herodiya, mkazi wa m’bale wake, komanso chifukwa cha zoipa zonse zimene Herode anachita,+