Mateyu 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Herode anagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+ Maliko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yohane ataponyedwa m’ndende, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu+ Maliko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Herodeyo anatumiza anthu kukagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende, chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+ Luka 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Herode anawonjezera choipa china pa zonsezo: Anatsekera Yohane m’ndende.+
3 Pakuti Herode anagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+
14 Tsopano Yohane ataponyedwa m’ndende, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu+
17 Pakuti Herodeyo anatumiza anthu kukagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende, chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+