Mateyu 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Herode anagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+ Luka 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno popeza kuti Yohane anadzudzula Herode wolamulira chigawo, pa nkhani yokhudza Herodiya, mkazi wa m’bale wake, komanso chifukwa cha zoipa zonse zimene Herode anachita,+
3 Pakuti Herode anagwira Yohane, kum’manga ndi kum’tsekera m’ndende chifukwa Herode anakwatira Herodiya, mkazi wa m’bale wake Filipo.+
19 Ndiyeno popeza kuti Yohane anadzudzula Herode wolamulira chigawo, pa nkhani yokhudza Herodiya, mkazi wa m’bale wake, komanso chifukwa cha zoipa zonse zimene Herode anachita,+