Mateyu 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano Yesu atatsiriza mawu amenewa, khamu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa+ ndi kaphunzitsidwe kake, Yohane 7:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Alondawo anayankha kuti: “Palibe munthu amene analankhulapo ngati iyeyu n’kale lonse.”+
28 Tsopano Yesu atatsiriza mawu amenewa, khamu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa+ ndi kaphunzitsidwe kake,