Maliko 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mmenemo anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake,+ chifukwa anali kuwaphunzitsa monga munthu wokhala ndi ulamuliro, osati monga alembi.+ Luka 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kumeneko anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake,+ chifukwa anali kulankhula ndi mphamvu za ulamuliro.+
22 Mmenemo anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake,+ chifukwa anali kuwaphunzitsa monga munthu wokhala ndi ulamuliro, osati monga alembi.+
32 Kumeneko anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake,+ chifukwa anali kulankhula ndi mphamvu za ulamuliro.+