Maliko 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ataona zimenezi, anthu onse anazizwa kwambiri moti anayamba kukambirana kuti: “Kodi chimenechi n’chiyani? N’chiphunzitso chatsopano! Ngakhale mizimu yonyansa akuilamula mwamphamvu, ndipo ikumumvera.”+
27 Ataona zimenezi, anthu onse anazizwa kwambiri moti anayamba kukambirana kuti: “Kodi chimenechi n’chiyani? N’chiphunzitso chatsopano! Ngakhale mizimu yonyansa akuilamula mwamphamvu, ndipo ikumumvera.”+