Maliko 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho Yesu anachiritsa ambiri amene anali kudwala matenda osiyanasiyana,+ ndipo anatulutsa ziwanda zambiri. Koma sanalole kuti ziwandazo zilankhule, chifukwa zinali kum’dziwa kuti ndi Khristu.+
34 Choncho Yesu anachiritsa ambiri amene anali kudwala matenda osiyanasiyana,+ ndipo anatulutsa ziwanda zambiri. Koma sanalole kuti ziwandazo zilankhule, chifukwa zinali kum’dziwa kuti ndi Khristu.+